Numeri 34:6 - Buku Lopatulika6 Kunena za malire a kumadzulo Nyanja Yaikulu ndiyo malire anu; ndiyo malire anu a kumadzulo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Kunena za malire a kumadzulo Nyanja Yaikulu ndiyo malire anu; ndiyo malire anu a kumadzulo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 “Malire anu akuzambwe akhale Nyanja Yaikulu ndi gombe lake. Ameneŵa ndiwo malire akuzambwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 “ ‘Malire anu a ku madzulo adzakhala ku gombe la Nyanja Yayikulu. Amenewo ndiwo adzakhale malire anu a ku madzulo. Onani mutuwo |