Numeri 34:8 - Buku Lopatulika8 kuchokera kuphiri la Hori mulinge polowera Hamati; ndipo kutuluka kwake kwa malire kudzakhala ku Zedadi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 kuchokera kuphiri la Hori mulinge polowera Hamati; ndipo kutuluka kwake kwa malire kudzakhala ku Zedadi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Kuchokera ku phiri la Horiko, mulembe malire kufikira ku chipata cha Hamati, ndipo mathero a malirewo akhale ku Zedadi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 ndi kuchokera ku phiri la Hori mpaka ku Lebo Hamati. Malirewa apite ku Zedadi, Onani mutuwo |