Numeri 34:23 - Buku Lopatulika23 Wa ana a Yosefe; wa fuko la ana a Manase, kalonga Haniyele mwana wa Efodi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Wa ana a Yosefe; wa fuko la ana a Manase, kalonga Haniyele mwana wa Efodi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Mwa ana a Yosefe, m'fuko la ana a Manase akhale Haniyele mwana wa Efodi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Hanieli mwana wa Efodi, mtsogoleri wochokera ku fuko la Manase, mwana wa Yosefe; Onani mutuwo |