Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 34:24 - Buku Lopatulika

24 Wa fuko la ana a Efuremu, kalonga Kemuwele mwana wa Sifutani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Wa fuko la ana a Efuremu, kalonga Kemuwele mwana wa Sifutani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 M'fuko la ana a Efuremu akhale Kemuwele mwana wa Sifutani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Kemueli mwana wa Sifitani, mtsogoleri wochokera ku fuko la Efereimu, mwana wa Yosefe.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 34:24
2 Mawu Ofanana  

Wa ana a Yosefe; wa fuko la ana a Manase, kalonga Haniyele mwana wa Efodi.


Wa fuko la ana a Zebuloni, kalonga Elizafani mwana wa Paranaki.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa