Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 34:22 - Buku Lopatulika

22 Wa fuko la ana a Dani, kalonga Buki mwana wa Yogili.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Wa fuko la ana a Dani, kalonga Buki mwana wa Yogili.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 M'fuko la ana a Dani akhale Buki mwana wa Yogili.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Buki mwana wa Yogili, mtsogoleri wochokera ku fuko la Dani;

Onani mutuwo Koperani




Numeri 34:22
3 Mawu Ofanana  

Ndipo anayandikiza, nati Tidzamangira zoweta zathu makola kuno, ndi ana athu mizinda;


Wa fuko la Benjamini, Elidadi mwana wa Kisiloni.


Wa ana a Yosefe; wa fuko la ana a Manase, kalonga Haniyele mwana wa Efodi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa