Numeri 34:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo mudzilembere malire a kum'mawa ochokera ku Hazara-Enani kunka ku Sefamu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo mudzilembere malire a kum'mawa ochokera ku Hazara-Enani kunka ku Sefamu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 “Mulembe malire anu akuvuma kuyambira ku Hazarenaniko mpaka ku Sefamu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 “ ‘Za malire anu a kummawa, mulembe mzere kuchokera ku Hazari-Enani mpaka kukafika ku Sefamu. Onani mutuwo |