Numeri 34:11 - Buku Lopatulika11 ndi malire adzatsika ku Sefamu kunka ku Ribula, kum'mawa kwa Aini; ndipo malire adzatsika, nadzafikira mbali ya nyanja ya Kinereti kum'mawa, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 ndi malire adzatsika ku Sefamu kunka ku Ribula, kum'mawa kwa Aini; ndipo malire adzatsika, nadzafikira mbali ya nyanja ya Kinereti kum'mawa, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Atsike kuchokera ku Sefamu mpaka ku Ribula, kuvuma kwa Aini. Atsikebe mpaka ku gombe la Nyanja ya Galilea, kuvuma, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Malirewo adzatsikire ku Sefamu mpaka ku Ribila cha kummawa kwa Aini ndi kupitirira mpaka ku matsitso a cha kummawa kwa Nyanja ya Kinereti. Onani mutuwo |