Numeri 32:9 - Buku Lopatulika9 Popeza atakwera kunka ku chigwa cha Esikolo, naona dziko, anafoketsa mtima wa ana a Israele, kuti asalowe dzikoli Yehova adawapatsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Popeza atakwera kunka ku chigwa cha Esikolo, naona dziko, anafoketsa mtima wa ana a Israele, kuti asalowe dzikoli Yehova adawapatsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Iwo atapita ku chigwa cha Esikolo, nakaona dzikolo, adatayitsa mtima Aisraele, pakuŵauza kuti asakaloŵe m'dziko limene Chauta adaŵapatsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Atapita ku chigwa cha Esikolo, ndi kuliona dzikolo, anafowoketsa Aisraeli kuti asalowe mʼdziko limene Yehova anawapatsa. Onani mutuwo |