Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 32:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Atapita ku chigwa cha Esikolo, ndi kuliona dzikolo, anafowoketsa Aisraeli kuti asalowe mʼdziko limene Yehova anawapatsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

9 Popeza atakwera kunka ku chigwa cha Esikolo, naona dziko, anafoketsa mtima wa ana a Israele, kuti asalowe dzikoli Yehova adawapatsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Popeza atakwera kunka ku chigwa cha Esikolo, naona dziko, anafoketsa mtima wa ana a Israele, kuti asalowe dzikoli Yehova adawapatsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Iwo atapita ku chigwa cha Esikolo, nakaona dzikolo, adatayitsa mtima Aisraele, pakuŵauza kuti asakaloŵe m'dziko limene Chauta adaŵapatsa.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 32:9
5 Mawu Ofanana  

Atafika ku chigwa cha Esikolo, anadulako nthambi ya mpesa ya phava limodzi la mphesa ndipo anthu awiri ananyamulizana, natenganso makangadza ndi nkhuyu.


Malo amenewo anawatcha chigwa cha Esikolo chifukwa cha phava la mphesa limene Aisraeli anadula kumeneko.


Ndipo atabwerako anapita kwa Mose ndi Aaroni ndi kwa Aisraeli onse ku Kadesi mʼchipululu cha Parani. Kumeneko anafotokozera anthu onse nawaonetsanso zipatso za mʼdzikolo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa