Numeri 32:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo Mose anati kwa ana a Gadi ndi ana a Rubeni, Kodi abale anu apite kunkhondo, ndi inu mukhale pansi kuno? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo Mose anati kwa ana a Gadi ndi ana a Rubeni, Kodi abale anu apite kunkhondo, ndi inu mukhale pansi kuno? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Koma Mose adafunsa ana a Gadi ndi ana a Rubeni kuti, “Kodi abale anu azikamenya nkhondo, inu mutangokhala kuno? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ndipo Mose anati kwa Agadi ndi Arubeni, “Kodi anthu a mtundu wanu apite ku nkhondo inu mutangokhala kuno? Onani mutuwo |