Numeri 32:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo anati, Ngati tapeza ufulu pamaso panu, mupatse anyamata anu dziko ili likhale laolao; tisaoloke Yordani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo anati, Ngati tapeza ufulu pamaso panu, mupatse anyamata anu dziko ili likhale laolao; tisaoloke Yordani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ngati mwatikomera mtima, mutipatse dzikoli atumiki anufe, kuti likhale lathu. Musatipititse patsidya pa Yordani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Iwo anati, ‘Ngati tapeza ufulu pamaso panu atumiki anufe, mutipatse dziko limeneli kuti likhale lathu. Tisawoloke nanu Yorodani.’ ” Onani mutuwo |