Numeri 32:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo mufoketseranji mtima wa ana a Israele kuti asaoloke ndi kulowa dzikoli Yehova anawapatsa? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo mufoketseranji mtima wa ana a Israele kuti asaoloke ndi kulowa dzikoli Yehova anawapatsa? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Chifukwa chiyani mufuna kuŵatayitsa mtima Aisraele, kuti asakaloŵe m'dziko limene Chauta adaŵapatsa? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Chifukwa chiyani mukufowoketsa Aisraeli kupita mʼdziko limene Yehova wawapatsa? Onani mutuwo |