Numeri 27:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo akapanda kukhala naye mwana wamkazi, mupatse abale ake cholowa chake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo akapanda kukhala naye mwana wamkazi, mupatse abale ake cholowa chake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Akakhala kuti alibe mwana wamkazi, choloŵa chakecho chikhale cha abale ake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ngati alibe mwana wamkazi, muzipereka cholowa chakecho kwa abale ake. Onani mutuwo |