Numeri 27:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo unene ndi ana a Israele, ndi kuti, Akafa munthu wamwamuna wopanda mwana wamwamuna, cholowa chake achilandire mwana wake wamkazi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo unene ndi ana a Israele, ndi kuti, Akafa munthu wamwamuna wopanda mwana wamwamuna, cholowa chake achilandire mwana wake wamkazi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ndipo uŵauze Aisraele kuti, ‘Munthu akafa opanda mwana wamwamuna, choloŵa chake chikhale cha mwana wake wamkazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 “Uza Aisraeli kuti, ‘Ngati munthu afa wosasiya mwana wamwamuna, muzipereka cholowa chake kwa mwana wake wamkazi. Onani mutuwo |