Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 27:8 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 “Uza Aisraeli kuti, ‘Ngati munthu afa wosasiya mwana wamwamuna, muzipereka cholowa chake kwa mwana wake wamkazi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

8 Ndipo unene ndi ana a Israele, ndi kuti, Akafa munthu wamwamuna wopanda mwana wamwamuna, cholowa chake achilandire mwana wake wamkazi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Ndipo unene ndi ana a Israele, ndi kuti, Akafa munthu wamwamuna wopanda mwana wamwamuna, cholowa chake achilandire mwana wake wamkazi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Ndipo uŵauze Aisraele kuti, ‘Munthu akafa opanda mwana wamwamuna, choloŵa chake chikhale cha mwana wake wamkazi.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 27:8
2 Mawu Ofanana  

“Zimene ana aakazi a Zelofehadi akunena ndi zoona. Uyenera kuwapatsadi cholowa chawo pakati pa abale a abambo awo ndipo uwapatse cholowa cha abambo awowo.


Ngati alibe mwana wamkazi, muzipereka cholowa chakecho kwa abale ake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa