Numeri 27:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo akapanda kukhala nao abale, mupatse abale a atate wake cholowa chake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo akapanda kukhala nao abale, mupatse abale a atate wake cholowa chake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Akakhala kuti alibe abale, choloŵa chakecho chikhale cha abale a bambo wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ngati alibe abale muzipereka cholowa chake kwa abale a abambo ake. Onani mutuwo |