Numeri 26:57 - Buku Lopatulika57 Ndipo awa ndi owerengedwa ao a Alevi monga mwa mabanja ao: Geresoni, ndiye kholo la banja la Ageresoni; Kohati, ndiye kholo la banja la Akohati; Merari, ndiye kholo la banja la Amerari. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201457 Ndipo awa ndi owerengedwa ao a Alevi monga mwa mabanja ao: Geresoni, ndiye kholo la banja la Ageresoni; Kohati, ndiye kholo la banja la Akohati; Merari, ndiye kholo la banja la Amerari. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa57 Potsata mabanja ao chiŵerengero cha Alevi chinali motere: Geresoni anali kholo la banja la Ageresoni. Kohati anali kholo la banja la Akohati. Merari anali kholo la banja la Amerari. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero57 Alevi omwe anawerengedwa monga mwa mafuko awo ndi awa: kuchokera mwa Geresoni, fuko la Ageresoni; kuchokera mwa Kohati, fuko la Akohati; kuchokera mwa Merari, fuko la Amerari. Onani mutuwo |