Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 26:57 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

57 Alevi omwe anawerengedwa monga mwa mafuko awo ndi awa: kuchokera mwa Geresoni, fuko la Ageresoni; kuchokera mwa Kohati, fuko la Akohati; kuchokera mwa Merari, fuko la Amerari.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

57 Ndipo awa ndi owerengedwa ao a Alevi monga mwa mabanja ao: Geresoni, ndiye kholo la banja la Ageresoni; Kohati, ndiye kholo la banja la Akohati; Merari, ndiye kholo la banja la Amerari.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

57 Ndipo awa ndi owerengedwa ao a Alevi monga mwa mabanja ao: Geresoni, ndiye kholo la banja la Ageresoni; Kohati, ndiye kholo la banja la Akohati; Merari, ndiye kholo la banja la Amerari.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

57 Potsata mabanja ao chiŵerengero cha Alevi chinali motere: Geresoni anali kholo la banja la Ageresoni. Kohati anali kholo la banja la Akohati. Merari anali kholo la banja la Amerari.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:57
12 Mawu Ofanana  

Ana aamuna a Levi ndi awa: Geresoni, Kohati ndi Merari.


Ana a Levi anali awa: Geresoni, Kohati ndi Merari.


Eliezara mwana wa Aaroni anakwatira mmodzi mwa ana aakazi a Putieli, ndipo anabereka Finehasi. Awa anali atsogoleri a mabanja a Levi, monga mwa mafuko awo.


Koma mabanja a fuko la Levi okha sanawawerenge pamodzi ndi ena.


Koma Alevi sanawawerenge pamodzi ndi Aisraeli enawo monga momwe Yehova analamulira Mose.


Cholowa chawo uchigawe pakati pa fuko lalikulu ndi lalingʼono mwa maere.”


“Werenga Alevi monga mwa mabanja awo ndi mafuko awo. Werenga mwamuna aliyense kuyambira wa mwezi umodzi kapena kupitirirapo.”


Mayina a ana aamuna a Levi ndi awa: Geresoni, Kohati ndi Merari.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa