Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 26:58 - Buku Lopatulika

58 Awa ndi mabanja a Alevi: banja la Alibini, banja la Ahebroni, banja la Amali, banja la Amusi, banja la Akora. Ndipo Kohati anabala Amuramu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

58 Awa ndi mabanja a Alevi: banja la Alibini, banja la Ahebroni, banja la Amali, banja la Amusi, banja la Akora. Ndipo Kohati anabala Amuramu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

58 Mabanja a Alevi anali aŵa: banja la Alibini, banja la Ahebroni, banja la Amahali, banja la Amusi, banja la Akora. Kohati anali bambo wa Amuramu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

58 Awanso anali mabanja a Alevi: banja la Alibini, banja la Ahebroni, banja la Amali, banja la Amusi, fuko la Kora banja la Akohati, (Kohati anali abambo a Amramu.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:58
6 Mawu Ofanana  

Ndipo Amuramu anadzitengera Yokebede mlongo wa atate wake akhale mkazi wake; ndipo anambalira Aroni ndi Mose; ndi zaka za moyo wa Amuramu ndizo zana limodzi mphambu makumi atatu kudza zisanu ndi ziwiri.


Ndipo ana aamuna a Kora ndiwo: Asiri ndi Elikana, ndi Abiyasafu; amenewo ndiwo mabanja a Akora.


Koma Kora, mwana wa Izihara, mwana wa Kohati, mwana wa Levi, anatenga Datani ndi Abiramu, ana a Eliyabu, ndi Oni mwana wa Peleti, ana a Rubeni;


Banja la Aamuramu, ndi banja la Aizihara, ndi banja la Ahebroni, ndi banja la Auziyele ndiwo a Kohati; ndiwo mabanja a Akohati.


Banja la Amali, ndi banja la Amusi ndiwo Amerari; ndiwo mabanja a Merari.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa