Numeri 26:44 - Buku Lopatulika44 Ana aamuna a Asere monga mwa mabanja ao ndiwo: Imina, ndiye kholo la banja la Aimina; Isivi, ndiye kholo la banja la Aisivi; Beriya, ndiye kholo la banja la Aberiya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201444 Ana amuna a Asere monga mwa mabanja ao ndiwo: Imina, ndiye kholo la banja la Imina; Isivi, ndiye kholo la banja la Aisivi; Beriya, ndiye kholo la banja la Aberiya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa44 Potsata mabanja ao ana aamuna a Asere anali aŵa: Imina, anali kholo la banja la Aimina. Isivi anali kholo la banja la Aisivi. Beriya anali kholo la banja la Aberiya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero44 Zidzukulu za Aseri monga mwa mafuko awo zinali izi: kuchokera mwa Imina, fuko la Aimuna; kuchokera mwa Isivi, fuko la Ayisivi; kuchokera mwa Beriya, fuko la Aberiya; Onani mutuwo |