Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 26:43 - Buku Lopatulika

43 Mabanja onse a Asuhamu monga mwa owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana anai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

43 Mabanja onse a Asuhamu monga mwa owerengedwa ao ndiwo zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu zinai kudza mazana anai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

43 Anthu oŵerengedwa pa mabanja onse a Suhamu adakwanira 64,400.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

43 Onse a fuko la Asuhamu amene anawerengedwa analipo 64,400.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:43
3 Mawu Ofanana  

Mwana wamwamuna wa Dani monga mwa mabanja ake ndiye Suhamu, ndiye kholo la banja la Asuhamu. Iwo ndiwo mabanja a Dani monga mwa mabanja ao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa