Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 26:44 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

44 Zidzukulu za Aseri monga mwa mafuko awo zinali izi: kuchokera mwa Imina, fuko la Aimuna; kuchokera mwa Isivi, fuko la Ayisivi; kuchokera mwa Beriya, fuko la Aberiya;

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

44 Ana aamuna a Asere monga mwa mabanja ao ndiwo: Imina, ndiye kholo la banja la Aimina; Isivi, ndiye kholo la banja la Aisivi; Beriya, ndiye kholo la banja la Aberiya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

44 Ana amuna a Asere monga mwa mabanja ao ndiwo: Imina, ndiye kholo la banja la Imina; Isivi, ndiye kholo la banja la Aisivi; Beriya, ndiye kholo la banja la Aberiya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

44 Potsata mabanja ao ana aamuna a Asere anali aŵa: Imina, anali kholo la banja la Aimina. Isivi anali kholo la banja la Aisivi. Beriya anali kholo la banja la Aberiya.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:44
4 Mawu Ofanana  

Ana aamuna a Aseri ndi awa: Imuna, Isiva, Isivi, Beriya ndi Sera mlongo wawo. Ana aamuna a Beriya ndi awa: Heberi ndi Malikieli.


Ana a Aseri anali awa: Imuna, Isiva, Isivi ndi Beriya. Mlongo wawo anali Sera.


Kuchokera mwa zidzukulu za Aseri: Amuna onse a zaka makumi awiri kapena kupitirirapo, omwe akanatha kugwira ntchito ya usilikali anawalemba mayina awo monga mwa mbiri ya mafuko awo ndi mabanja awo.


ndipo kupyolera mwa zidzukulu za Beriya: kuchokera mwa Heberi, fuko la Aheberi; kuchokera mwa Malikieli, fuko la Amalikieli;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa