Numeri 26:45 - Buku Lopatulika45 Ana a Beriya ndiwo: Hebere, ndiye kholo la banja la Ahebere; Malikiele, ndiye kholo la banja la Amalikiele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201445 Ana a Beriya ndiwo: Hebere, ndiye kholo la banja la Ahebere; Malikiele, ndiye kholo la banja la Amalikiele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa45 Ana aamuna a Beriya anali aŵa: Hebere anali kholo la banja la Ahebri. Malikiele anali kholo la banja la Amalikiele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero45 ndipo kupyolera mwa zidzukulu za Beriya: kuchokera mwa Heberi, fuko la Aheberi; kuchokera mwa Malikieli, fuko la Amalikieli; Onani mutuwo |