Numeri 26:16 - Buku Lopatulika16 Ozini, ndiye kholo la banja la Aozini; Eri, ndiye kholo la banja la Aeri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ozini, ndiye kholo la banja la Aozini; Eri, ndiye kholo la banja la Aeri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Ozini anali kholo la banja la Aozini. Eri anali kholo la banja la Aeri. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 kuchokera mwa Ozini, fuko la Aozini; kuchokera mwa Eri, fuko la Aeri; Onani mutuwo |