Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 26:15 - Buku Lopatulika

15 Ana aamuna a Gadi monga mwa mabanja ao ndiwo: Zefoni, ndiye kholo la banja la Azefoni; Hagi, ndiye kholo la banja la Ahagi; Suni, ndiye kholo la banja la Suni;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Ana amuna a Gadi monga mwa mabanja ao ndiwo: Zefoni, ndiye kholo la banja la Azefoni; Hagi, ndiye kholo la banja la Ahagi; Suni, ndiye kholo la banja la Suni;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 Potsata mabanja ao ana aamuna a Gadi anali aŵa: Zefoni anali kholo la banja la Azefoni. Hagi anali kholo la banja la Ahagi. Suni anali kholo la banja la Asuni.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Zidzukulu za Gadi mwa mafuko awo ndi izi: kuchokera mwa Zefoni, fuko la Azefoni; kuchokera mwa Hagi, fuko la Ahagi; kuchokera mwa Suni, fuko la Asuni;

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:15
6 Mawu Ofanana  

Ndi ana aamuna a Gadi: Zifiyoni, ndi Hagi, ndi Suni, ndi Eziboni, ndi Eri, ndi Arodi, ndi Areli.


Ndi ana a Gadi anakhala pandunji pao m'dziko la Basani mpaka Saleka:


A ana a Gadi, kubadwa kwao, monga mwa mabanja ao, powerenga maina, kuyambira a zaka makumi awiri ndi mphambu, onse akutulukira kunkhondo;


Ndi fuko la Gadi; kalonga wa ana a Gadi ndiye Eliyasafu mwana wa Reuwele.


Iwo ndiwo mabanja a Asimeoni, zikwi makumi awiri mphambu ziwiri kudza mazana ziwiri.


Ozini, ndiye kholo la banja la Aozini; Eri, ndiye kholo la banja la Aeri;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa