Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 26:16 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 kuchokera mwa Ozini, fuko la Aozini; kuchokera mwa Eri, fuko la Aeri;

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

16 Ozini, ndiye kholo la banja la Aozini; Eri, ndiye kholo la banja la Aeri;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 Ozini, ndiye kholo la banja la Aozini; Eri, ndiye kholo la banja la Aeri;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 Ozini anali kholo la banja la Aozini. Eri anali kholo la banja la Aeri.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 26:16
3 Mawu Ofanana  

Ana aamuna a Gadi ndi awa: Zifioni, Hagi, Suni, Eziboni, Eri, Arodi ndi Areli.


Zidzukulu za Gadi mwa mafuko awo ndi izi: kuchokera mwa Zefoni, fuko la Azefoni; kuchokera mwa Hagi, fuko la Ahagi; kuchokera mwa Suni, fuko la Asuni;


kuchokera mwa Arodi, fuko la Aarodi; kuchokera mwa Arieli, fuko la a Areli.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa