Numeri 24:3 - Buku Lopatulika3 Pamenepo ananena fanizo lake, nati, Balamu mwana wa Beori anenetsa, ndi munthuyo anatsinzina maso anenetsa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pamenepo ananena fanizo lake, nati, Balamu mwana wa Beori anenetsa, ndi munthuyo anatsinzina maso anenetsa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 ndipo adayamba kulankhula mau auneneri, adati, “Mau a Balamu mwana wa Beori, mau a munthu amene maso ake ndi otsekuka, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 ndipo ananena uthenga wake: “Uthenga wa Balaamu mwana wa Beori, uthenga wa amene diso lake ndi lotsekuka, Onani mutuwo |