Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 24:12 - Buku Lopatulika

12 Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Kodi sindinauzanso amithenga anu amene munawatumiza kwa ine, ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Kodi sindinauzanso amithenga anu amene munawatumiza kwa ine, ndi kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Balamu adafunsa Balaki kuti “Kodi amithenga anu amene mudaŵatuma kwa ine aja, sindidaŵauze kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Balaamu anayankha Balaki kuti, “Kodi sindinawawuze amithenga amene munawatumiza kwa ine,

Onani mutuwo Koperani




Numeri 24:12
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Balamu anayankha nati kwa anyamata a Balaki, Chinkana Balaki andipatsa nyumba yake yodzala ndi siliva ndi golide, sindikhoza kutumpha mau a Yehova Mulungu wanga, kuchepsako kapena kuonjezako.


Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Taonani, ndafika kwa inu; ngati ndili nayo mphamvu konse tsopano kunena kanthu? Mau amene Mulungu aike m'kamwa mwanga ndiwo ndidzanena.


Chifukwa chake thawira ku malo ako tsopano; ndikadakuchitira ulemu waukulu; koma, taona, Yehova wakuletsera ulemu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa