Numeri 24:11 - Buku Lopatulika11 Chifukwa chake thawira ku malo ako tsopano; ndikadakuchitira ulemu waukulu; koma, taona, Yehova wakuletsera ulemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Chifukwa chake thawira ku malo ako tsopano; ndikadakuchitira ulemu waukulu; koma, taona, Yehova wakuletsera ulemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Nchifukwa chake, chokani, kazipitani kwanu. Ndidaakuuzani kuti ndidzakupatsani mphotho, koma Chauta wakana kuti muilandire mphothoyo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tsopano choka msanga uzipita kwanu! Ndinanena kuti ndidzakulipira bwino kwambiri, koma Yehova sanafune kuti ulandire malipirowo.” Onani mutuwo |