Numeri 23:9 - Buku Lopatulika9 Pakuti, pokhala pamwamba pa matanthwe ndimpenya, pokhala pa zitunda ndimuyang'ana; taonani, ndiwo anthu akukhala pa okha. Osadziwerengera pakati pa amitundu ena. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pakuti, pokhala pamwamba pa matanthwe ndimpenya, pokhala pa zitunda ndimuyang'ana; taonani, ndiwo anthu akukhala pa okha. Osadziwerengera pakati pa amitundu ena. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pamene ndikuŵaona kuchokera pamwamba pa phiri, pamene ndikuŵayang'ana kuchokera ku mapiri, ndikuwona anthu okhala paokha, osadziŵerengera kumodzi ndi mitundu ina. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Kuchokera pamwamba pa mapiri ndikuona anthu, ndikuwaona kuchokera pa zitunda. Ndikuona anthu okhala pawokha, osakhala mʼgulu limodzi ndi mitundu ina. Onani mutuwo |