Numeri 23:10 - Buku Lopatulika10 Adzawerenga ndani fumbi la Yakobo, kapena kuwerenga limodzi la magawo anai la Israele? Ndipo ine ndife monga amafa oongoka mtima, chitsiriziro changa chifanane nacho chake! Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Adzawerenga ndani fumbi la Yakobo, kapena kuwerenga limodzi la magawo anai la Israele? Ndipo ine ndife monga amafa oongoka mtima, chitsiriziro changa chifanane nacho chake! Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ndani angathe kuŵerenga zidzukulu, zidzukulu za Yakobe zochuluka ngati fumbi, kapena kuŵerenga ngakhale chimodzi mwa zigawo zinai za fuko lonse la Israele? Lekeni ine ndife imfa ya anthu amene mudaŵalungamitsa, matsiriziro anga akhale onga a anthu amenewo.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndani angawerenge zidzukulu za Yakobo zochuluka ngati fumbi, kapena chimodzi mwa zigawo zinayi za Israeli? Lekeni ndife imfa ya oyera mtima, ndi chimaliziro changa chikhale ngati chawo!” Onani mutuwo |