Numeri 23:11 - Buku Lopatulika11 Pamenepo Balaki anati kwa Balamu, Wandichitiranji? Ndinakutenga utemberere adani anga, ndipo taona, wawadalitsa ndithu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Pamenepo Balaki anati kwa Balamu, Wandichitiranji? Ndinakutenga utemberere adani anga, ndipo taona, wawadalitsa ndithu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Balaki adafunsa Balamu kuti, “Mwandichitira zotani? Suja ndidakuitanani kuti mudzatemberere adani anga, koma m'malo mwake mwangoŵadalitsa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Balaki anati kwa Balaamu, “Wandichitira chiyani? Ndinakuyitana kuti utemberere adani anga, ndipo taona, sunachite chilichonse koma kuwadalitsa!” Onani mutuwo |