Numeri 23:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo anayankha nati, Chimene achiika m'kamwa mwanga Yehova, sindiyenera kodi kunena ichi? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo anayankha nati, Chimene achiika m'kamwa mwanga Yehova, sindiyenera kodi kunena ichi? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Iye adayankha kuti, “Kodi sindiyenera kulankhula zokhazo zimene Chauta adaika m'kamwa mwanga?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Iye anayankha kuti, “Kodi sindinayenera kuyankhula zimene Yehova anandiwuza?” Onani mutuwo |