Numeri 23:8 - Buku Lopatulika8 Ndidzatemberera bwanji amene Mulungu sanamtemberere? Ndidzanyoza bwanji, amene Yehova sanamnyoze? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndidzatemberera bwanji amene Mulungu sanamtemberere? Ndidzanyoza bwanji, amene Yehova sanamnyoze? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Koma ine ndingathe bwanji kumtemberera amene Mulungu sadamtemberere? Ndingathe bwanji kumufunira zoipa amene Chauta sadamfunire zoipa? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ndingatemberere bwanji amene Mulungu sanawatemberere? Ndinganyoze bwanji amene Yehova sanawanyoze? Onani mutuwo |