Numeri 23:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo ananena fanizo lake, nati, Ku Aramu ananditenga Balaki, mfumu ya Mowabu ananditenga ku mapiri a kum'mawa, Idza, udzanditembererere Yakobo. Idza, nudzanyoze Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo ananena fanizo lake, nati, Ku Aramu ananditenga Balaki, mfumu ya Mowabu ananditenga ku mapiri a kum'mawa, Idza, udzanditembererere Yakobo. Idza, nudzanyoze Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Apo Balamu adayamba kulankhula mau auneneri, adati, “Balaki mfumu ya ku Mowabu yandiitana kuchokera ku Aramu, ku mapiri akuvuma, kuti, ‘Bwerani, dzatemberereni Yakobe m'malo mwanga, bwerani mudzamfunire Israele zoipa.’ Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Ndipo Balaamu ananena uthenga wake: “Balaki ananditenga kuchoka ku Aramu, mfumu ya ku Mowabu kuchokera ku mapiri a kummawa. Iye anati, ‘Bwera, temberera Yakobo mʼmalo mwanga, pita nyoza Israeli.’ Onani mutuwo |