Numeri 23:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo anabwerera kwa iye, ndipo, taonani, analikuima pa nsembe yopsereza yake, iye ndi akalonga onse a Mowabu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo anabwerera kwa iye, ndipo, taonani, analikuima pa nsembe yopsereza yake, iye ndi akalonga onse a Mowabu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Balamu adabwerera kwa Balaki, nampeza iyeyo pamodzi ndi akalonga onse a Amowabu ataima pafupi ndi nsembe yake yopsereza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ndipo anabwerera kwa iye namupeza atayima pafupi ndi nsembe yake pamodzi ndi akuluakulu onse a Mowabu. Onani mutuwo |