Numeri 22:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Balaki mwana wa Zipori anaona zonse Israele anachitira Aamori. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Balaki mwana wa Zipori anaona zonse Israele anachitira Aamori. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Balaki mwana wa Zipora adaona zonse zimene Aisraele adachita Aamori. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Tsono Balaki mwana wa Zipori anaona zonse zimene Aisraeli anachitira Aamori, Onani mutuwo |