Numeri 22:3 - Buku Lopatulika3 Ndipo Mowabu anachita mantha akulu ndi anthuwo, popeza anachuluka; nada mtima Mowabu chifukwa cha ana a Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Ndipo Mowabu anachita mantha akulu ndi anthuwo, popeza anachuluka; nada mtima Mowabu chifukwa cha ana a Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Amowabu adaopa anthuwo kwambiri, chifukwa anali ambirimbiri. Amowabu adachitadi mantha ndi Aisraele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 ndipo Amowabu anaopa anthuwo chifukwa analipo ambiri. Amowabuwo anachita mantha kwambiri mpaka ananjenjemera chifukwa cha Aisraeli. Onani mutuwo |