Numeri 22:1 - Buku Lopatulika1 Ndipo ana a Israele anayenda ulendo, namanga mahema m'zigwa za Mowabu, tsidya la Yordani ku Yeriko. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndipo ana a Israele anayenda ulendo, namanga mahema m'zigwa za Mowabu, tsidya la Yordani ku Yeriko. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Aisraele adanyamuka ulendo nakamanga mahema ao m'zigwa za Amowabu patsidya pa Yordani ku Yeriko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Aisraeli anayenda kupita ku zigwa za Mowabu nakamanga misasa yawo tsidya lina la Yorodani moyangʼanana ndi Yeriko. Onani mutuwo |