Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 22:2 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Tsono Balaki mwana wa Zipori anaona zonse zimene Aisraeli anachitira Aamori,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

2 Ndipo Balaki mwana wa Zipori anaona zonse Israele anachitira Aamori.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Ndipo Balaki mwana wa Zipori anaona zonse Israele anachitira Aamori.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Balaki mwana wa Zipora adaona zonse zimene Aisraele adachita Aamori.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 22:2
4 Mawu Ofanana  

Yehova anamva pempho la Aisraeli ndipo anapereka Akanaaniwo kwa iwo. Anawawononga pamodzi ndi mizinda yawo. Kotero malowo anatchedwa Horima.


Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, analimbana ndi Israeli. Iye anayitanitsa Balaamu mwana wa Beori kuti akutemberereni.


Kodi ndinu abwino kuposa Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu? Kodi iye anakanganapo kapena kuchita nkhondo ndi Israeli?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa