Numeri 21:12 - Buku Lopatulika12 Pochokapo anayenda ulendo, namanga mahema m'chigwa cha Zeredi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pochokapo anayenda ulendo, namanga mahema m'chigwa cha Zeredi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Atachoka kumeneko, adakamanga m'chigwa cha Zeredi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Kuchoka kumeneko anayendabe nakamanga misasa yawo mʼchigwa cha Zeredi. Onani mutuwo |