Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 21:11 - Buku Lopatulika

11 Ndipo anachoka ku Oboti, namanga mahema ku Iyeabarimu, m'chipululu chakuno cha Mowabu, kotulukira dzuwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Ndipo anachoka ku Oboti, namanga mahema ku Iyeabarimu, m'chipululu chakuno cha Mowabu, kotulukira dzuwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Ndipo adachoka ku Oboti nakamanga ku Iyeabarimu m'chipululu choyang'anana ndi Mowabu, kuvuma.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Kenaka anasamuka ku Oboti nakamanga misasa yawo ku Iye-Abarimu, mʼchipululu chimene chili kummawa kwa Mowabu, kotulukira dzuwa.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 21:11
4 Mawu Ofanana  

Pamenepo ana a Israele anayenda ulendo, namanga mahema mu Oboti.


Pochokapo anayenda ulendo, namanga mahema m'chigwa cha Zeredi.


Nachokera ku Punoni, nayenda namanga mu Oboti.


Nachokera ku Oboti, nayenda namanga mu Iyeabarimu, m'malire a Mowabu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa