Numeri 21:10 - Buku Lopatulika10 Pamenepo ana a Israele anayenda ulendo, namanga mahema mu Oboti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Pamenepo ana a Israele anayenda ulendo, namanga mahema m'Oboti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Aisraele adanyamukanso, nakamanga mahema ao ku Oboti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Aisraeli anayendabe nakamanga misasa yawo ku Oboti. Onani mutuwo |