Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 21:12 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Kuchoka kumeneko anayendabe nakamanga misasa yawo mʼchigwa cha Zeredi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

12 Pochokapo anayenda ulendo, namanga mahema m'chigwa cha Zeredi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Pochokapo anayenda ulendo, namanga mahema m'chigwa cha Zeredi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Atachoka kumeneko, adakamanga m'chigwa cha Zeredi.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 21:12
4 Mawu Ofanana  

Kenaka anasamuka ku Oboti nakamanga misasa yawo ku Iye-Abarimu, mʼchipululu chimene chili kummawa kwa Mowabu, kotulukira dzuwa.


Atachoka ku Iye-Abarimu anakamanga ku Diboni Gadi.


“Tsopano nyamukani, muwoloke khwawa la Arinoni. Taona ndapereka mʼmanja mwako Sihoni Mwamori mfumu ya Hesiboni ndi dziko lake lonse. Yambapo kutenga chuma chake ndi kumenyana naye nkhondo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa