Numeri 20:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Mose anatenga ndodoyo kuichotsa pamaso pa Yehova, monga Iye anamuuza iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Mose anatenga ndodoyo kuichotsa pamaso pa Yehova, monga Iye anamuuza iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pamenepo Mose adatenga ndodo imene inali pamaso pa Chauta, monga momwe Iyeyo adamlamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Choncho Mose anatenga ndodo pamaso pa Yehova monga momwe anamulamulira. Onani mutuwo |