Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 20:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Choncho Mose anatenga ndodo pamaso pa Yehova monga momwe anamulamulira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

9 Ndipo Mose anatenga ndodoyo kuichotsa pamaso pa Yehova, monga Iye anamuuza iye.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo Mose anatenga ndodoyo kuichotsa pamaso pa Yehova, monga Iye anamuuza iye.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Pamenepo Mose adatenga ndodo imene inali pamaso pa Chauta, monga momwe Iyeyo adamlamulira.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 20:9
3 Mawu Ofanana  

Nyamula ndodo yako ndi kutambasula dzanja lako kuloza ku nyanja, kugawa madzi kuti Aisraeli awoloke powuma.


Kotero Mose anatenga mkazi wake ndi ana ake aamuna, ndipo anawakweza pa bulu nayamba ulendo wobwerera ku Igupto. Ndipo anatenga ndodo ya Mulungu ija mʼdzanja lake.


Yehova anawuza Mose kuti, “Bwezera ndodo ya Aaroni patsogolo pa Bokosi la Umboni, kuti chikhale chizindikiro cha kuwukira kwawo. Zimenezi zidzathetsa kudandaula kwawo kotsutsana nane, kuopa kuti angafe.”


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa