Numeri 20:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Mose ndi Aroni anasonkhanitsa msonkhano pathanthwe, nanena nao iye, Tamvanitu, opikisana naye inu; kodi tikutulutsireni madzi m'thanthwe umu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Mose ndi Aroni anasonkhanitsa msonkhano pathanthwe, nanena nao iye, Tamvanitu, opikisana naye inu; kodi tikutulutsireni madzi m'thanthwe umu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Tsono Mose ndi Aroni adasonkhanitsa mpingo wonse pamodzi kuthanthweko nauza anthuwo kuti, “Imvani anthu opandukanu. Kodi tichite kukutulutsirani madzi m'thanthwemu?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Mose ndi Aaroni anasonkhanitsa anthuwo pamodzi ku thanthwelo ndipo Mose anawawuza kuti, “Tamverani osamvera inu, kodi tikupatseni madzi kuchokera ku thanthwe ili?” Onani mutuwo |