Numeri 2:26 - Buku Lopatulika26 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 ndipo ankhondo ake ngokwanira 62,700. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 62,700. Onani mutuwo |