Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 2:27 - Buku Lopatulika

27 Ndipo iwo akumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a fuko la Asere; ndi kalonga wa ana a Asere ndiye Pagiyele mwana wa Okarani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

27 Ndipo iwo a kumanga mahema ao poyandikizana naye ndiwo a fuko la Asere; ndi kalonga wa ana a Asere ndiye Pagiyele mwana wa Okarani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

27 Amene amange pafupi ndi fuko lake akhale a fuko la Asere, limene mtsogoleri wake ndi Pagiyele mwana wa Okarani,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

27 Fuko la Aseri lidzamanga pafupi ndi iwowo. Mtsogoleri wa Aaseri ndi Pagieli mwana wa Okirani.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 2:27
5 Mawu Ofanana  

Wa Asere, Pagiyele mwana wa Okarani.


Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi asanu ndi limodzi mphambu ziwiri kudza mazana asanu ndi awiri.


Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi anai mphambu chimodzi kudza mazana asanu.


Tsiku la khumi ndi limodzi kalonga wa ana a Asere, ndiye Pagiyele mwana wa Okarani;


ndi nsembe yoyamika, ng'ombe ziwiri nkhosa zamphongo zisanu, atonde asanu, anaankhosa asanu a chaka chimodzi; ndicho chopereka cha Pagiyele mwana wa Okarani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa