Numeri 2:28 - Buku Lopatulika28 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi anai mphambu chimodzi kudza mazana asanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201428 Ndi khamu lake, ndi owerengedwa ake, ndiwo zikwi makumi anai mphambu chimodzi kudza mazana asanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa28 ndipo ankhondo ake ngokwanira 41,500. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero28 Chiwerengero cha gulu lake lankhondo ndi 41,500. Onani mutuwo |